Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #272
Hymn 272 Ponya Cingwe Ca Moyo
[V1]
THROW OUT THE LIFE-LINE 1. Pabvuta pa Nyanja, ponya cingwe,
Pali mbale apulumutsidwe;
Mbale wa mnzathu, ndani angathe
Kuponya cingweco, kumpulumutsa.
THROW OUT THE LIFE-LINE 1. Pabvuta pa Nyanja, ponya cingwe,
Pali mbale apulumutsidwe;
Mbale wa mnzathu, ndani angathe
Kuponya cingweco, kumpulumutsa.
[C]
Ponya cingweco! Cingwe ca moyo!
Alikunka ndi madzi!
Ponya cingweco! Cingwe ca moyo!
Wina amira lero.
2. Ponya cingweco mofulumira;
Ucedweranji ndi kujejema?
Ana amira, fulumiratu,
Ukampumulutse msanga, msangatu.
3. Ponya anthuwo azunzikatu,
Atatha koopsa sungafike;
Mphepo zabvuto ndi za matsoka.
Msanga ziwatsitsa kwakuya kwa bi.
4. Nyengo yowapulumutsa itha,
Atifera posacedwea pano;
Kangaza mbale usacedwetse,
Ingoponya cingwe apulumuke.
Ponya cingweco! Cingwe ca moyo!
Alikunka ndi madzi!
Ponya cingweco! Cingwe ca moyo!
Wina amira lero.
2. Ponya cingweco mofulumira;
Ucedweranji ndi kujejema?
Ana amira, fulumiratu,
Ukampumulutse msanga, msangatu.
3. Ponya anthuwo azunzikatu,
Atatha koopsa sungafike;
Mphepo zabvuto ndi za matsoka.
Msanga ziwatsitsa kwakuya kwa bi.
4. Nyengo yowapulumutsa itha,
Atifera posacedwea pano;
Kangaza mbale usacedwetse,
Ingoponya cingwe apulumuke.