Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #273
Hymn 273 Tsamira Pa Manja A Yesu
[V1]
LEAN ON HIS ARMS 1. Tsamira pa manja a Yesu, Akuthangate athagata;
Ukamkhulupira ndithu, Adzakusangalatsa.

[C]
(Sop. & Tenor):
Tsamiratu m’cikondi cace; Tsamiratu, yesa cifundo;
Tsamiratu, yang’ana m’Mwamba, Tsamira Mpulumutsi.
(Bass & Alto):
Tsamiratu Iye, m’cikondi cace, Tsamira Iye, yesa cifuno;
Tsamiratu Iyel, yang’ana m’Mwamba, Tsamira Mpulumutsi.
2. Tsamira pa manja a Yesu, ’Dzauza njira adzauza;
Ingotsala mokondwera, pomvera mau ace.
3. Tsamira pa manja a Yesu, ’Dzakusamala, kusamala!
Katundu wolemeretsa Mpereke kwa Ambuye.
4. Tsamira pa manja a Yesu, Msiyire zonse, zonsezodi!
Mtima wace ngwacikondi, Maso ace sasinza.