Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #67
Hymn 67 Idzani Nonsenu Okonda Yesu
[V1]
Idzani nonsenu, Okonda Yesuyo,
Tiyimbe nyimbo yabwino, Tiyimbe nyimbo yabwino
Ku mpando wakewo, Ku mpando wakewo.

[C]
Tiyende (tu) pamodzi, Tilikupita kumwamba;
Akhristu tilikupita (pita), ku Ziyoni wabwinoyo.

[V2]
Ngakhale enawo Aleke kwimbako,
Akhristu ’fe tidzayimba, Akhristu ’fe tidzayimba
Kumlemekeza ’Ye, Kumlemekeza ’Ye.

[V3]
Akhristu tonsefe, Tikondwe mdzikoli,
Koposa anthu enawo, Koposa anthu enawo,
Tisanafikeko, Tisanafikeko.

[V4]
Tiyimbe mokondwa, Misozi iume;
Poyenda kunka kwathuko, Poyenda kunka kwathuko,
Kwa Mlungu wathuyo, Kwa Mlungu wathuyo.