Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #180
Hymn 180 Sitidziwa Nthawi Ya Kudza
[V1]
Sitidziwa nthawi yakudza kwa Mbuye,
Koma zooneka pa dziko zinena
Adzabwera msanga, tikondwa,
Komatu sitidziwa nthawi.
Sitidziwa nthawi yakudza kwa Mbuye,
Koma zooneka pa dziko zinena
Adzabwera msanga, tikondwa,
Komatu sitidziwa nthawi.
[C]
Adzatu! Tikonzeke, tilinde!
Adzatu! Aleluya! Aleluya!
Adza ndi mphamvu za ’Tate wake,
Komatu sitidziwa nthawi.
Adzatu! Tikonzeke, tilinde!
Adzatu! Aleluya! Aleluya!
Adza ndi mphamvu za ’Tate wake,
Komatu sitidziwa nthawi.
[V2]
Ku’nika kulipo kwa anthu a nzeru,
Cho’nadi chilipo mu mau a Mlungu,
Alembi anena momveka,
Komatu sitidziwa nthawi.
Ku’nika kulipo kwa anthu a nzeru,
Cho’nadi chilipo mu mau a Mlungu,
Alembi anena momveka,
Komatu sitidziwa nthawi.
[C]
Adzatu! Tikonzeke, tilinde!
Adzatu! Aleluya! Aleluya!
Adza ndi mphamvu za ’Tate wake,
Komatu sitidziwa nthawi.
Adzatu! Tikonzeke, tilinde!
Adzatu! Aleluya! Aleluya!
Adza ndi mphamvu za ’Tate wake,
Komatu sitidziwa nthawi.
[V3]
Tilinde, tipemphe ndi nyali zowala,
Tigwirenso ntchito mpakatu abwera.
Poona zozizwa tiyimbe,
Komatu sitidziwa nthawi.
Tilinde, tipemphe ndi nyali zowala,
Tigwirenso ntchito mpakatu abwera.
Poona zozizwa tiyimbe,
Komatu sitidziwa nthawi.
[C]
Adzatu! Tikonzeke, tilinde!
Adzatu! Aleluya! Aleluya!
Adza ndi mphamvu za ’Tate wake,
Komatu sitidziwa nthawi.
Adzatu! Tikonzeke, tilinde!
Adzatu! Aleluya! Aleluya!
Adza ndi mphamvu za ’Tate wake,
Komatu sitidziwa nthawi.