Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #78
Hymn 78 Kupulumutsa Omwe Ali Kufa
[V1]
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Uwachotse m’manda a uchimo;
Lilira ochimwa, nuwadzutsetu,
Nuwauze za Yesu Mbuyeyo.
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Uwachotse m’manda a uchimo;
Lilira ochimwa, nuwadzutsetu,
Nuwauze za Yesu Mbuyeyo.
[C]
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Yesu wachifundo alanditsa.
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Yesu wachifundo alanditsa.
[V2]
Ngakhale amkana, Iye alinda,
Afuna kulandira olapa.
Awapembedzera moona Mtima,
Adzawakhululukira iwo.
Ngakhale amkana, Iye alinda,
Afuna kulandira olapa.
Awapembedzera moona Mtima,
Adzawakhululukira iwo.
[C]
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Yesu wachifundo alanditsa.
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Yesu wachifundo alanditsa.
[V3]
Mu Mtima wa munthu muli zambiri,
Koma Yesu azichotsa zonse;
Atakhudzidwa ndi chikondi chake,
Nsinga za Satana zidzaduka.
Mu Mtima wa munthu muli zambiri,
Koma Yesu azichotsa zonse;
Atakhudzidwa ndi chikondi chake,
Nsinga za Satana zidzaduka.
[C]
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Yesu wachifundo alanditsa.
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Yesu wachifundo alanditsa.
[V4]
Pulumutsa omwe ali kufatu
Limbitsa othodwa ndi olema;
Kwabwezera m’njira yopapatiza,
Ndi kuwauza za Mpulumutsi
Pulumutsa omwe ali kufatu
Limbitsa othodwa ndi olema;
Kwabwezera m’njira yopapatiza,
Ndi kuwauza za Mpulumutsi
[C]
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Yesu wachifundo alanditsa.
Pulumutsa omwe ali kufatu,
Yesu wachifundo alanditsa.