Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #271
Hymn 271 Nkana Chimo Nlalikuru
[V1]
THO’ YOUR SINS BE AS SCARLET 1. Nkana chimo nlikuru, lingakanganulidwe;
Nkana chino nlikuru, lingakanganulidwe;
Nkana chimo ngori’ra, ayeretsedwa;
Nkana chimo nlikuru, Nkana chimo nlikuru,
Lingakanganulidwe; Lingakanganulidwe.
2. Imva liu lipempha, "Bweranso kwa Mlunguyo;"
Imva liu lipempha, "Bweranso kwa Mlunguyo."
Ali ndi nsisi zambiri, ndi cikondico.
Imva liu lipempha, Imva liu lipempha,
"Bweranso kwa Mlunguyo: Bweranso kwa Mlunguyo."
3. Akukhululukira, sadzakumbukiranso;
Akukhululukira, sadzakumbukiranso;
"Ndiyang’aneni anthuni," ati Mbuyeyo
Akukhululukira, Akukhulukira,
Sadzakumbukiranso, Sadzakumbukiranso.