Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #65
Hymn 65 N’kwabwino Kukhulupirira
[V1]
N’kwabwino kukhulupira, M’mau ake a Yesu;
Kupuma m’malonjezo’ke, Ndimtama nthawi zonse.

[C]
Ndikhulupirira Yesu, Ndimtama nthawi zonse;
Yesu ali wa chifundo, Ndimtama nthawi zonse.

[V2]
N’kwabwino kukhulupira, Mwazi wake wa Yesu;
Kungomkhulupira Iye Adzatitsuka ife.

[V3]
N’kwabwino kukhulupira, Kuti achotse tchimo;
Nadzatipatsa’fe moyo, Chimwemwe ndi mtendere.

[V4]
Ndikondwa kumdziwa Iye, Mpulumutsi wangayo;
N’dziwa adzakhala nane, Mpaka chimaliziro.