Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #66
Hymn 66 Poyambapo Ndakondwadi
[V1]
Poyambapo ndakondwadi, Ntapeza Inu Mbuyetu,
Ndiyimba nyimbo yomweyi, Kukondwa sindikhala du.

[C]
Kalelo! Kalelo! Wandisambitsa mmtimamo;
Wandiweruza lomwelo, Kupemba ndi kukondwako.
Kalelo! Kalelo! Wandisambitsa mmtimamo.

[V2]
Ndamuza ndimakhalatu Ku nyumba kwake komweko;
Mnyamata wake ndinetu, Ndampatsa Mtima wonsewo.

[V3]
Omwewo mapanganowo, Sitilekana ifetu.
Ndamvera ine mauwo, Wandiloleza m’mtimamo.

[V4]
Ndampatsa mtima wonsewo, Kupuma mwa Ambuyeyo:
Ndikhala, osamlekai, Kuthawa ndi kumsiya ’Ye.