Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #64

Hymn 64 Kodi Walemedwa M’mtima Mwako?

[V1]
Kodi walemedwa m’mtima mwako?
Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu
Kodi uli kumva za chisoni?
Nena kwa Yesu yekha.

[C]
Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu,
Ndi bwenzi labwinotu.
Ndiye bwenzi lopambana onse,
Nena kwa Yesu yekha.

[V2]
Kodi ukulira mwa chisoni?
Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu;
Kodi tchimo lina labisika?
Nena kwa Yesu yekha.

[C]
Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu,
Ndi bwenzi labwinotu.
Ndiye bwenzi lopambana onse,
Nena kwa Yesu yekha.

[V3]
Kodi umaopa za chisoni?
Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu;
Kodi ulikuda nkhawa m’mtima?
Nena kwa Yesu yekha.

[C]
Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu,
Ndi bwenzi labwinotu.
Ndiye bwenzi lopambana onse,
Nena kwa Yesu yekha.

[V4]
Kodi ukulingalira imfa?
Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu;
Kodi ukulira kuti adze?
Nena kwa Yesu yekha.

[C]
Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu,
Ndi bwenzi labwinotu.
Ndiye bwenzi lopambana onse,
Nena kwa Yesu yekha.

64. Kodi Walemedwa M’mtima Mwako?

Link copied to clipboard successfully!