Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #40

Hymn 40 Poyenda Ndi Mbuye

[V4]
Sitingadziwetu zachikondi chake, Mpaka titadziperekatu;
Chifukwa chifundo ndi chimwemwe chake, Amapatsa anthu omvera.

5. Pompo m’chiyanjano tidzakhala naye, Kapena kuyenda ndi Iye;
Ndipo tidzachita chifuniro chake, Tidzakhala omvera ndithu.

[C]
1. Poyenda ndi Mbuye, mkuwala kwakeko, Aunikira m’njira mwathu;
Pakugwira ntchito amakhala nafe, Ndi onse amene amvera.


Khulupira, palibenso njira, Yakukondwa mwa Yesu,
Komatu kumvera.

2. Mthunzi sungagwetu, pena mtambo mmwamba, Komatu azipirikitsa;
Nkhawa ndi chisoni zidzachoka ngati, Tikhulupira ndi kumvera.

3. Chifukwa cha ntchito ndi zisoni zathu, Adzatilipira mokwana;
Kopandanso imfa, kapena kukwiya, Tidzadalitsika pomvera.

40. Poyenda Ndi Mbuye

Link copied to clipboard successfully!