Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #10
Hymn 10 Kodi Tidzasonkhanadi?
[V1]
SHALL WE GATHER 1. Kodi tidzasonkhanadi, Pali mtsinjewo wa moyo,
Wakuyenda nthawi zonse, Kwa Mulungu m’mwambamo.

[C]
Inde, tikomane komwe, Ku mtsinje wakukoma wa Mulungu;
Tisangane ndi olungama. Pa mtsinje m’mwambambo.
2. Pa magombe a pa mtsinje, Tidzayendayenda komwe;
Tidzalemekeza Mlungu, Nthawi zonse zonsezo.
3. Tisanadze pa magombe, Tidzatula akatundu.
Yesu adzatilandira, ’Dzativeka tonsefe.
4. Msanga tikomane komwe, Potsiriza pa ulendo,
Msanga tidzakondwerabe, Timyimbira Mlunguyo.