Hymn 3 Maso Ndi Maso

[V1]
FACE TO FACE1 Maso ndi maso ndi Khristu, Kodi ndidzachitanji?
Mmene ndidzaona Yesu, Yemwe anandifera.

[C]

N’dzamona maso ndi maso, Kuseri kwa mitambo;
Posachedwa ndidzamona, Mulemerero wace!

2 Tsopano ndimona Iye, Mwa chizimezimetu,
Tsiku lija ndidzaona, Ulemerero wache.

3 Pamene zowawa zonse, Nthenda ndi imfa zitha,
Dziko likadzakonzedwa, Ndidzakondwa koposa!

[V4]
Lodala tsikulo m’mene! Ndidzamuona Yesu,
Mpulumutsi wanga yemwe, Anandikonda ine.

[C]

N’dzamona maso ndi maso, Kuseri kwa mitambo;
Posachedwa ndidzamona, Mulemerero wace!

2 Tsopano ndimona Iye, Mwa chizimezimetu,
Tsiku lija ndidzaona, Ulemerero wache.

3 Pamene zowawa zonse, Nthenda ndi imfa zitha,
Dziko likadzakonzedwa, Ndidzakondwa koposa!

3. Maso Ndi Maso

Link copied to clipboard successfully!