Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #259
Hymn 259 Tidzakomana Kodi?
[V1]
SHALL WE MEET? 1. Tidzakomana patsidya, Mafunde akadzatha?
Kowala kosalekeza, Kulibe cisoninso?
SHALL WE MEET? 1. Tidzakomana patsidya, Mafunde akadzatha?
Kowala kosalekeza, Kulibe cisoninso?
[C]
Tidzakomanako? Tidzakomane patsidya?
Tikakomane patsidya, Mabvuto akadzatha?
2. Tikakomana padoko, Akadzatha mabvuto?
Tidzaiponya nangula Pagombe lokomalo?
3. Tikakomana m’mudzimo; Nyumba zonyezimira,
Makomanso nga yasipi, omangidwa ndi Mbuye?
4. Tikakomana ndi Yesu Potenga anthu ace;
Ubwino tidzaudziwa Ntakhala mu mpando’ce.