Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #11
Hymn 11 Ndidzakutsatani
[V1]
I WILL FOLLOW THEE 1. Ndidzakutsatani Mbuye, Kuli konse mupita;
Ndidzakutsatani Mbuye, Inde n’dzakutsatani.

[C]
Ndidzakutsatani Mbuye, Yemwe munandifera;
Ngakhale akukaneni, Ndidzakutsatani ’Nu.
2. Nkana njira ndi ya minga Yopanda matakadzo,
Mukandikonzera Ine, Mokondwa n’dzatsata ’nu.
3. Nkana chisautso chidza, Kapena ndiyesedwa;
Mbuyenso anayesedwa, Ndidzamtsata mokondwa.
4. Nkana ndipeze mavuto, Sindidzakukanani;
Mnazunzidwanso koopsa Ndidzatsatabe Inu.
5. M’mafunde ndi mozamamo, Mudzanditsogolera;
M’nayenda m’mafunde kale, Ndidzakutsatani ’Nu.