Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #168
Hymn 168 Yehova Ndi M’busa Wanga
[V1]
Yehova ndi Mbusa, Sin’dzasowai,
Ndigona ku busa La msipu Wake
Anditsogolera Ku madzi ake,
Anditsitsimutsa Ndi mphamvu Yake.
Yehova ndi Mbusa, Sin’dzasowai,
Ndigona ku busa La msipu Wake
Anditsogolera Ku madzi ake,
Anditsitsimutsa Ndi mphamvu Yake.
[V2]
Anditsogolera M’mabande mwake,
Chifukwa cha dzina Lokondedwalo.
Ngakhale ndiyenda Pafupi imfa,
Ha! sindidzaopa Zoipa zonse.
Anditsogolera M’mabande mwake,
Chifukwa cha dzina Lokondedwalo.
Ngakhale ndiyenda Pafupi imfa,
Ha! sindidzaopa Zoipa zonse.
[V3]
Chibonga ndi ndodo Za Mbusa wanga
Zindisangalatsa Masiku onse.
Mundiyalikira Pa maso panga,
Mkuona kwa mdani Chakudya changa.
Chibonga ndi ndodo Za Mbusa wanga
Zindisangalatsa Masiku onse.
Mundiyalikira Pa maso panga,
Mkuona kwa mdani Chakudya changa.
[V4]
Mudzoza mafuta Pa mutu panga,
Mwadzaza chifundo Mu chikho changa,
Udzanditsatira Ukoma wanu,
Ndidzakhala nanu Masiku onse.
Mudzoza mafuta Pa mutu panga,
Mwadzaza chifundo Mu chikho changa,
Udzanditsatira Ukoma wanu,
Ndidzakhala nanu Masiku onse.