Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #33
Hymn 33 Mulungu Atsogoza ’Ne
[V1]
HE LEADETH ME1. Mulungu atsogoza ’ne, Ndapuma m’mtima mwangamo.
Ayang’anira m’njiramo, Poyenda ine konseko.

[C]
Mulungu atsogoza ’ne, Ndi dzanja-dzanja lakelo.
Ndidzamtsatira Mbuyanga, Poyenda ine konseko.

[V2]
Masiku ena mdima bi, Ndimavutika m’mtimamo.
Pa nthawi zina nkondwadi, Popeza zokondwetsazo.

[V3]
Ndzagwira dzanja lanulo, Osang’ung’udza konseyi,
Ndidzanka mokondweratu, Pomtsata Mbuye wangayo.

[V4]
Podzatha ntchito yangayi, Podzagonjetsa tchimolo,
Kumene ndidzakhalatu, Sindidzaopa imfayo.