Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #63

Hymn 63 Ndingayere Bwanji ’Ne?

[V1]
Ndingayere bwanji ’ne? Mwazi wa Ambuye Yesu.
Nch’ani chindichizanso? Mwazi wa Ambuye Yesu.

[C]
Mtsinje wa mwaziwo, Undiyeretsanso;
Sin’dziwa winanso, Mwazi wa Ambuye ndiwo.

[V2]
Pakudetswa ndiona, Mwazi wa Ambuye yesu.
Pakuchimwa nditchula, Mwazi wa Ambuye Yesu

[C]
Mtsinje wa mwaziwo, Undiyeretsanso;
Sin’dziwa winanso, Mwazi wa Ambuye ndiwo.

[V3]
Zina sizikwanatu, Mwazi wa Ambuye ndiwo.
Ntchito zanga zichepa, Mwazi wa Ambuye ndiwo.

[C]
Mtsinje wa mwaziwo, Undiyeretsanso;
Sin’dziwa winanso, Mwazi wa Ambuye ndiwo.

[V4]
Ndimakhulupiradi, Mwazi wa Ambuye Yesu.
Zolungama zangazi, Mwazi wa Ambuye Yesu.

[C]
Mtsinje wa mwaziwo, Undiyeretsanso;
Sin’dziwa winanso, Mwazi wa Ambuye ndiwo.

[V5]
Poyamika ndiyimba Mwazi wa Ambuye Yesu.
Ndithokoza Mbuyanga, Mwazi wa Ambuye Yesu.

[C]
Mtsinje wa mwaziwo, Undiyeretsanso;
Sin’dziwa winanso, Mwazi wa Ambuye ndiwo.

63. Ndingayere Bwanji ’Ne?

Link copied to clipboard successfully!