Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #62

Hymn 62 Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

[V1]
Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu,
Ndisiya zoipa chifukwa chanu;
Ambuye wabwino ndi Mplumutsiyo;
Ndikonda tsopano koposa kale.

[V2]
Ndikonda chifukwa munakonda ’ne;
Mnafera pa mtengo kuombola ’ne;
Mukhululukira zoipa zonse;
Ndikonda tsopano koposa kale.

[V3]
Ndidzakukondani kosalekai,
Ndidzakutamani masiku onse.
Mpakatu ndidzafa ndidzanenabe,
Ndikonda tsopano koposa kale.

[V4]
Ku malo owalo kumwamba komwe
Ndidzakuongani, Ambuye Yesu;
Ntavala korona ndizayimbabe,
Ndikonda tsopano koposa kale.

62. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Link copied to clipboard successfully!