Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #118

Hymn 118 Ati Yesu Mbuyeyo

[V1]
Ati Yesu Mbuyeyo, Ofo’ka ndinutu,
Mudikire, mpemphedi, Ndidzapatsa mphamvutu,

[C]
Yesu wathadi Za mangawatu,
Inde, ndinaipa bii, Watsuka ine mbu.

[V2]
Mbuye ndimva leroli Za mphamvu zanuzi,
Zokha zisandutsadi Mtima wanga woti bii.

[C]
Yesu wathadi Za mangawatu,
Inde, ndinaipa bii, Watsuka ine mbu.

[V3]
Ine kanthu ndilibe, Kogula moyowu,
Ndingotsuka mtimano M’mwazi wa Ambuye ’Nu.

[C]
Yesu wathadi Za mangawatu,
Inde, ndinaipa bii, Watsuka ine mbu.

[V4]
Mmene ndidzaimatu Pa chiweruzopo,
Podzapulumukatu, Ndidzamtama Yesuyo.

[C]
Yesu wathadi Za mangawatu,
Inde, ndinaipa bii, Watsuka ine mbu.

118. Ati Yesu Mbuyeyo

Link copied to clipboard successfully!