Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #42
Hymn 42 Sitidzalekananso
[V1]
WITH FRIENDS ON EARTH1. Tikakhala ndi abwenzitu, M’dziko lathu lino,
Posachedwa timalekana Nao mwa chisoni.
WITH FRIENDS ON EARTH1. Tikakhala ndi abwenzitu, M’dziko lathu lino,
Posachedwa timalekana Nao mwa chisoni.
[C]
Sitidzalekana m’mwamba, Sitidzalekana,
M’dziko lokometsetsalo, Sitidzalekana.
Sitidzalekana m’mwamba, Sitidzalekana,
M’dziko lokometsetsalo, Sitidzalekana.
[V2]
Timakhala ndi ch’yembekezo, Pakufa anzathu,
Kuti pakutha dziko lino, Tidzakhala nao.

[V3]
Sitidzalekananso ai, M’dziko lokomalo,
Nyimbo za chimwemwe, mtendere, ’Dzayimba kosatha.