Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #41
Hymn 41 Mulungu Akhala Ndi Inu
[V1]
Mulungu akhale ndi inu, Mpaka tidzaonananso;
Atsogoze, asunge ’nu; Mulungu akhale ndi inu.
Mulungu akhale ndi inu, Mpaka tidzaonananso;
Atsogoze, asunge ’nu; Mulungu akhale ndi inu.
[C]
Asunga nonsenu, Tikomana ndi Yesu,
Asunga nonsenu, Mulungu akhale ndi inu.
Asunga nonsenu, Tikomana ndi Yesu,
Asunga nonsenu, Mulungu akhale ndi inu.
[V2]
Mulungu akhale ndi inu, Ndi mapiko akubisa,
Masiku onse kudyetsa; Mulungu akhale ndi inu.

[V3]
Mulungu akhale ndi inu, Ndi pamene muvutika,
Adzakuthangatani ’nu, Mulungu akhale ndi inu.

[V4]
Mulungu akhale ndi inu, Ndi chikondi chake chonse,
Asunge mzoopsya zonse, Mulungu akhale ndi inu.