Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #39

Hymn 39 Thanthwe Lolimba

[V1]
Chiyembekezo changatu, Chili mwa Yesu Woyera
Sindikhulupira wina Koma dzina la Yesuyo.

[V4]
Pamene Iye adzadza, Ndidzapezeke mwa Iye,
Ndiri m’chilungamo chake, Wopanda naye chifukwa.

39. Thanthwe Lolimba

Link copied to clipboard successfully!