Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #288
Hymn 288 Anadzatu Kwa Yesu
[V1]
THEY BROUGHT THEIR GIFTS TO JESUS 1. Anadzatu kwa Yesu ndi mphatso zaozo,
Ndi Mtima wa cikondi Natula zonsezo
Zokoma Mtima ntchito Zothandizanatu,
Ndi zopereka zao Ndizo za mtengotu.
THEY BROUGHT THEIR GIFTS TO JESUS 1. Anadzatu kwa Yesu ndi mphatso zaozo,
Ndi Mtima wa cikondi Natula zonsezo
Zokoma Mtima ntchito Zothandizanatu,
Ndi zopereka zao Ndizo za mtengotu.
[C]
Tulani mphatso zanu kwa Yesu Mbuyeyo
Pereka Mtima wanu Pa guwa lacelo.
2. Pakati pa opatsa Naima mlendoyo
Naona anthu ena Napatsa zaozo,
Naye nalakalaka Kupatsa zacezo,
Analibetu kanthu Kopatsa Mbuyeyo.
3. Nalira, Mbuye wanga, Wokoma Mtima ’Nu,
Tengani Mtima wanga Wodzadza chimolo
Ambuye namuyankha Usati yachepa;
Yakoyo, mwana wanga Yaposa zonsezo.
Tulani mphatso zanu kwa Yesu Mbuyeyo
Pereka Mtima wanu Pa guwa lacelo.
2. Pakati pa opatsa Naima mlendoyo
Naona anthu ena Napatsa zaozo,
Naye nalakalaka Kupatsa zacezo,
Analibetu kanthu Kopatsa Mbuyeyo.
3. Nalira, Mbuye wanga, Wokoma Mtima ’Nu,
Tengani Mtima wanga Wodzadza chimolo
Ambuye namuyankha Usati yachepa;
Yakoyo, mwana wanga Yaposa zonsezo.