Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #287
Hymn 287 M’Mayesoro Anga
[V1]
IN THE HOUR OF TRIAL 1. M’mayesero anga, Tate mndisunge;
Ndisakukaneni, Kukusiyani,
Pondenguma ine, Kumbukireni,
Nsalekene nanu, Musanditaye.
2. Za dziko nzacabe, Ndisatengeke
Cuma ca poyera, Cisandikope
Kusunga kwani sisi, Ndikubvomera
Ndikana zoipa zolakalaka.
3. Matsoka si anu, Zolabadira;
Zowawa zikadza Kusokonzeza;
Zikumphanitu Ndisacimwe bi;
Nkhawa zanga zonse, Ndikupatsani.
IN THE HOUR OF TRIAL 1. M’mayesero anga, Tate mndisunge;
Ndisakukaneni, Kukusiyani,
Pondenguma ine, Kumbukireni,
Nsalekene nanu, Musanditaye.
2. Za dziko nzacabe, Ndisatengeke
Cuma ca poyera, Cisandikope
Kusunga kwani sisi, Ndikubvomera
Ndikana zoipa zolakalaka.
3. Matsoka si anu, Zolabadira;
Zowawa zikadza Kusokonzeza;
Zikumphanitu Ndisacimwe bi;
Nkhawa zanga zonse, Ndikupatsani.