Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #276
Hymn 276 M’khola Mwa Ng’ombe
[V1]
JESUS, MY SAVIOUR, TO BETHELEHEM CAME 1. M’kola mwa ng’ombe mu Betlemumo, anabadwa ambuyangawo
Etu, ndidziwa, natsikirako, Kufuna inetu
Afuna inetu, afuna inetu.
Etu, ndizizwa, natsikirako, Afuna inetu.
2. Popacikidwa pa Kalvarepo, Yesu anandiombolerako,
Inde, ndidziwa, nakondaneko, Nafera inetu.
Nafera inetu, Nafera inetu.
Inde ndizizwa nakondaneko, Nafera inetu.
3. Mbusa wokoma ndi Mbuyangayo, Nandiitana posocerapo,
Konse koipa nalondaneko, Kubweza inetu
Abweza inetu, abweza inetu
Konse koipa nalondaneko, Abwenza inetu.
4. Uko kumwamba, Mbuyangayo, Nandikonzera mokhaliramo,
Tsiku linalo adzabweranso, Kutenga inetu
Atenga inetu, atenga inetu.
Tsiku linalo adzabweranso, Kutenga inetu.