Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #277

Hymn 277 Tsogolere Muuni

[V1]
LEAD KINDLY LIGHT 1. Tsogolere muuni mu mdima, Tsogolere;
Kwada ndiri kutari ndi kwathu; Tsogolere
Sindipempha kuona za m’tari,
Phazi langa limodzi likwana

2. Sindinali wotere wokhoza kupemphera;
Ndisankha njira’nga; Tsogolere;
Ndinakonda zinthu zacibwana, Tsogolere;
Ndinanyada, musazikumbuke

3. Mphamvu yanu yandidalitsadi; Intsogoza
Mu malo monse moipa mpaka mdima watha;
M’mawa ’ngelo andisekerera;
Amenewo ndawakonda kale.

277. Tsogolere Muuni

Link copied to clipboard successfully!