Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #260
Hymn 260 Dambo La Byula
[V1]
VALE OF BEULAH 1. Ndipitira kunsi kwa dambo la cipululu,
Liri dambo lokongola lochedwa la Byula
Koma ndapezanso monse momera maluwa,
Mpulumutsi mwini wace ayenda ndi ine.
2. Palibe mthunzi wotsiriza panjira panga,
Kuunika kwa ulemerero kuwalitsa;
Am’mwamba andiyimbira nyimbo zokongola,
Apokolezana bwino kundicingamira.
3. Ndiri kunka ndi nsangala ku mzinda wowala,
Nsangalazo ziwalitsa njira tsiku ntsiku;
Ndasendeza zipata za mzinda wakuwala
Khwalalalo lindifitsa mzinda wa cikondi.