Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #237

Hymn 237 Akristu Limbikani!

[V1]
STAND UP! STAND UP FOR JESUS! 1. Akristu limbikani, imani mtimanji!
Mbendera nyamulani, musanthenthemerebi.
Wotsogolera wathu ndi Mwana wa Mulungu;
Adzagonjetsa onse, adani athuwo.

2. Tigwire nkhondo yomwe ya Mbuye wathuyo;
Ticotse zakuipa zokhala mtimamo.
Sitikwanira tokha kuleka zinthu zomwe;
Koma Mbuyathu Yesu atithangatatu.

3. Tsopano timenyana ndi zakuipazo,
Pamene nkhondo yatha tidzanka kwathuko;
Yesu adzalandira ankhondo ace onse,
Adzakhalitsa naye Kumwamba komweko.

4. Limbikani anzathu! Msanga nkhondo itha
Lero kuli cinkhondo, mawa tigonjetsa
Kwa iye wolakika, adzakhala moyo;
Pamodzi ndi Mfumuyo ’dzakhala kosatha.

237. Akristu Limbikani!

Link copied to clipboard successfully!