Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #238

Hymn 238 Akulowa M’zipata

[V1]
SWEEPING THROUGH THE GATES 1. Awa ndani pa tsidya la Nyanja, Omwe payola manda acetu,
Akondwera mwa Yesu? Asamba m’mwazi Wace.

[C]

Akulowa mzinda wa Yerusalemu,
Asamba m’mazi (wace) wa nkhosa;
Alowa m’zipata za Yerusalemu,
Asamba m’mwazi Wace.

2. Awa ndiwo anapeza Yesu, Pamene anali anyamata,
Nalandira cisomo, Asamba m’mwazi Wace.

3. Awa ndiwo mansautso yao, Anapeza kupuma mwa Yesu,
Mtendere mu mtimamo, Asamba m’mwazi Wace.

4. Iwo adapirira mabvuto, Anapyola pakati pa moto:
Yesu ati idzani, Asamba m’mwazi Wace.

238. Akulowa M’zipata

Link copied to clipboard successfully!