Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #225

Hymn 225 Uyang’ane Mdaniyo

[V1]
STAND LIKE THE BRAVE 1. Mkhristuwe dzuka! Alamula Mbuye;
Tenga cikopa, ndi lupanga m’dzanja,
Ukomane naye, usamuope
Ulimbe Mtima, Myang’ane mdaniyo.

Refrain:
Limba Mtima, Limba Mtima,
Limba Mtima, Pom’yang’ana mdani.

2. Zoopsa ziripo, ucenjeretu,
Usafulatire, ungapwekekwe;
Unyinji wa ’dani, udzagonjetsa,
Ulimbe Mtima, M’yang’ane mdaniyo.

3. Ntchito ya Mbuyako uiteteze;
Dzukatu mwa cangu nkhondoyo ithe;
Akakulamula, pita mwa cangu,
Ulimbe Mtima M’yang’ane mdaniyo.

4. Pita limbikira, suli wekhai,
Mwayi apatsa, cisangalatsonso;
Mwayi apatsa, cisangalatsonso;
Cikondi cace ngati mtsinje m’tengo;
Ulimbe Mtima M’yang’ane mdaniyo

225. Uyang’ane Mdaniyo

Link copied to clipboard successfully!