Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #224
Hymn 224 Nyali Yanu Iwalire
[V1]
LET THE LOWER LIGHTS BE BURNING 1. Tate wathu wa Kumwamba, ’Natipatsa nyali’Ce,
Koma atiuza ife, Tiwalitse enawo.
LET THE LOWER LIGHTS BE BURNING 1. Tate wathu wa Kumwamba, ’Natipatsa nyali’Ce,
Koma atiuza ife, Tiwalitse enawo.
[C]
Nyali yanu iwalire, Kusonyeza njirayo
Kwa ocimwa ndi ofo’ka, Njira yonka m’Mwambamo.
2. Kuli mdima m’dziko lino, Ndi namondwe wa bvuto,
Obvutika alindira Nyali yotsogozayo.
3. Konza nyali yako msanga, Pena wobvutikayo
Atayidwa mu mdima, Akapanda nyaliyo.