Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #226
Hymn 226 Pafupi Kukopeka
[V1]
ALMOST PERSUADED 1. Pang’onong’ono kukopedwa;
Pang’onong’ono kumlandira,
Wina akutero, "Pita, Mzimu, pita,
Ndikaona nthawi n’kuitana."
2. Pang’onong’ono, lero idza;
Pang’onong’ono usalubze,
Yesu akwitana, angelo mpafupi,
Anthu akupempha, Bweranitu.
3. Pangonong’ono mwayi wathaa;
Pang’onong’ono tsoka ladza!
Kucedwa simwayi, ndi tsoka loopsa.
Ha, adaliradi, "Ndacedwatu!"
ALMOST PERSUADED 1. Pang’onong’ono kukopedwa;
Pang’onong’ono kumlandira,
Wina akutero, "Pita, Mzimu, pita,
Ndikaona nthawi n’kuitana."
2. Pang’onong’ono, lero idza;
Pang’onong’ono usalubze,
Yesu akwitana, angelo mpafupi,
Anthu akupempha, Bweranitu.
3. Pangonong’ono mwayi wathaa;
Pang’onong’ono tsoka ladza!
Kucedwa simwayi, ndi tsoka loopsa.
Ha, adaliradi, "Ndacedwatu!"