Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #199

Hymn 199 Ulemu Kwa Mulungu

[V1]
Ulemu kwa Mlungu, Ambuye wathu,
Akonda, napatsa ’fe Mwana Wake;
Napatsatu moyo kuombola ’fe,
Pa khomo la moyo natsegulatu.

[C]
Tamani Mbuyeyo, Dziko limvere ’Ye;
Tamani Mbuyeyo, Anthu akondwetu;
Idzani kwa ’Tate mwa Mwana Wake,
Mpatseni ulemu anakonda ’fe.

[V2]
Anapulumutsa ndi mwazi Wake
Amene akhulupirira mwa ’Ye.
Ngakhale wochimwa koposa ndithu,
Adzakhululukidwa mwa Yesuyo.

[C]
Tamani Mbuyeyo, Dziko limvere ’Ye;
Tamani Mbuyeyo, Anthu akondwetu;
Idzani kwa ’Tate mwa Mwana Wake,
Mpatseni ulemu anakonda ’fe.

[V3]
Anatiphunzitsa zopambanazo,
Tikondwa mwa Yesu, Ambuye wathu;
Komabe ’dzazizwa kopambanadi,
Pamene atenga ’fe, kumwambako.

[C]
Tamani Mbuyeyo, Dziko limvere ’Ye;
Tamani Mbuyeyo, Anthu akondwetu;
Idzani kwa ’Tate mwa Mwana Wake,
Mpatseni ulemu anakonda ’fe.

199. Ulemu Kwa Mulungu

Link copied to clipboard successfully!