Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #200
Hymn 200 Ndinu Wakuyera!
[V1]
Ndinu wakuyera! Wa mphamvu zonse,
Nthawi ya m’mamawa tiyimba nyimboyi;
Mlengi wachifundo tikuyamikani,
Ee, Mlungu m’modzi mwa Atatuwo.
Ndinu wakuyera! Wa mphamvu zonse,
Nthawi ya m’mamawa tiyimba nyimboyi;
Mlengi wachifundo tikuyamikani,
Ee, Mlungu m’modzi mwa Atatuwo.
[V2]
Ndinu wakuyera! Onse pa dziko
Akuyimbirani nakupempherani;
Akumwamba omwe nagwadira Inu,
Wa chikhalire ndi wosafai.
Ndinu wakuyera! Onse pa dziko
Akuyimbirani nakupempherani;
Akumwamba omwe nagwadira Inu,
Wa chikhalire ndi wosafai.
[V3]
Ndinu wakuyera! Ife ochimwa,
Ulemero wanu sitimaona bi!
Mwayeradi nokha, wina saoneka;
Wangwiro m’mphamvu ndi m’kuyeramo.
Ndinu wakuyera! Ife ochimwa,
Ulemero wanu sitimaona bi!
Mwayeradi nokha, wina saoneka;
Wangwiro m’mphamvu ndi m’kuyeramo.