Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #103

Hymn 103 Anadza Kwa Yesu Mkuru Wina

[V1]
Anadza kwa Yesu mkuru wina, Kufunsa za njira ya chipulumutso;
Nayankha momveka Ambuyathuyo, Mukabadwensotu.

[C]
Mukabadwensotu, mukabadwensotu;
Indetu ndinenadi kwa inuyo, Mukabadwensotu.

[V2]
Nonsenu mverani mau ake Amene Ambuye nanena Kwa ‘ye,
Msanyozetu mau a uthengawu, Mukabadwensotu.

[C]
Mukabadwensotu, mukabadwensotu;
Indetu ndinenadi kwa inuyo, Mukabadwensotu.

[V3]
Mufuna kulowa mmwamba kodi? Kuyimba pamodzi ndi odalawo?
Mukafuna moyo wa nthawi zonse, Mukabadwensotu.

[C]
Mukabadwensotu, mukabadwensotu;
Indetu ndinenadi kwa inuyo, Mukabadwensotu.

103. Anadza Kwa Yesu Mkuru Wina

Link copied to clipboard successfully!