Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #195
Hymn 195 Tifuna Mzimu wanuyo
[V1]
Tifuna Mzimu wanuyo,
Yemwe nawala kalelo;
Nawatenthetsa m’mtimamo,
Nawalimbitsa mzo’psamo.
Tifuna Mzimu wanuyo,
Yemwe nawala kalelo;
Nawatenthetsa m’mtimamo,
Nawalimbitsa mzo’psamo.
[V2]
Mzimuyo ali kuti ko,
Nadzazayo Abramuyo?
Namsintha mtima Paulo,
Yemwe nampatsa changucho?
Mzimuyo ali kuti ko,
Nadzazayo Abramuyo?
Namsintha mtima Paulo,
Yemwe nampatsa changucho?
[V3]
Yemwenso kalekalelo
Nanena za chikondicho,
Nawala pa Yesayayo,
Nampatsa Daniel nzeruzo.
Yemwenso kalekalelo
Nanena za chikondicho,
Nawala pa Yesayayo,
Nampatsa Daniel nzeruzo.
[V4]
Kodi mulibe mphamvuzo
Monga Eliya nazimva?
Mose nawala nkhopeyo,
Yobu anapiriranso?
Kodi mulibe mphamvuzo
Monga Eliya nazimva?
Mose nawala nkhopeyo,
Yobu anapiriranso?
[V5]
M’chitetu monga kalelo,
Dzutsani ntchito yanuyo.
M’mene tipempha kwanuko,
Mtitsanulire Mzimuyo.
M’chitetu monga kalelo,
Dzutsani ntchito yanuyo.
M’mene tipempha kwanuko,
Mtitsanulire Mzimuyo.