Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #196
Hymn 196 Ufuna Kuomboledwa Kodi?
[V1]
Ufuna kuwomboledwa kodi?
Ilipo mphamvu m’mwazi Wake;
Ufuna kugonjetsa zoipa?
Muli mphamvu m’mwazi Wake.
Ufuna kuwomboledwa kodi?
Ilipo mphamvu m’mwazi Wake;
Ufuna kugonjetsa zoipa?
Muli mphamvu m’mwazi Wake.
[C]
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Yesuyo;
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Mwana wa Nkhosa.
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Yesuyo;
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Mwana wa Nkhosa.
[V2]
Ufuna kuleka kunyadako?
Ilipo mphamvu m’mwazi Wake;
Idzatu pa mtanda nutsukidwe,
Muli mphamvu m’mwazi Wake.
Ufuna kuleka kunyadako?
Ilipo mphamvu m’mwazi Wake;
Idzatu pa mtanda nutsukidwe,
Muli mphamvu m’mwazi Wake.
[C]
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Yesuyo;
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Mwana wa Nkhosa.
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Yesuyo;
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Mwana wa Nkhosa.
[V3]
Ufuna kuyera kopambana?
Ilipo mphamvu m’mwazi Wake;
Zoipa zonse adzayeretsa,
Muli mphamvu m’mwazi Wake.
Ufuna kuyera kopambana?
Ilipo mphamvu m’mwazi Wake;
Zoipa zonse adzayeretsa,
Muli mphamvu m’mwazi Wake.
[C]
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Yesuyo;
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Mwana wa Nkhosa.
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Yesuyo;
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Mwana wa Nkhosa.
[V4]
Ufuna kugwira ntchito Yake?
Ilipo mphamvu m’mwazi Wake;
Ufuna kumuyimbira Iye?
Muli mphamvu m’mwazi Wake.
Ufuna kugwira ntchito Yake?
Ilipo mphamvu m’mwazi Wake;
Ufuna kumuyimbira Iye?
Muli mphamvu m’mwazi Wake.
[C]
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Yesuyo;
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Mwana wa Nkhosa.
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Yesuyo;
Muli mphamvu (m’mwazi) yozizwitsatu,
M’mwazi wa Mwana wa Nkhosa.