Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #179
Hymn 179 Wakukonzeka Pakubwera Mkwati?
[V1]
Wakonzeka pakubwera Mkwatiyo, Mkwatiyo?
Wakonzeka pakubwera Mkwatiyo, Mkwatiyo?
Onani adza; onani adza;
Konzeka akubwera Mkwatiyo.
Wakonzeka pakubwera Mkwatiyo, Mkwatiyo?
Wakonzeka pakubwera Mkwatiyo, Mkwatiyo?
Onani adza; onani adza;
Konzeka akubwera Mkwatiyo.
[C]
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Yang’ana adza, yang’ana adza!
Konzeka akubwera Mkwatiyo.
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Yang’ana adza, yang’ana adza!
Konzeka akubwera Mkwatiyo.
[V2]
Konzetsani nyali zanu, adzatu, adzatu!
Konzetsani nyali zanu, adzatu, adzatu!
Akudza msanga; akudza msanga;
Konzeka moyo wanga wonse ’we.
Konzetsani nyali zanu, adzatu, adzatu!
Konzetsani nyali zanu, adzatu, adzatu!
Akudza msanga; akudza msanga;
Konzeka moyo wanga wonse ’we.
[C]
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Yang’ana adza, yang’ana adza!
Konzeka akubwera Mkwatiyo.
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Yang’ana adza, yang’ana adza!
Konzeka akubwera Mkwatiyo.
[V3]
Tidzakakomana naye, Mkwatiyo, Mkwatiyo!
Tidzakakomana naye, Mkwatiyo, Mkwatiyo!
Adzadi Yesu; adzadi Yesu;
Tidzakomana naye Mkwatiyo.
Tidzakakomana naye, Mkwatiyo, Mkwatiyo!
Tidzakakomana naye, Mkwatiyo, Mkwatiyo!
Adzadi Yesu; adzadi Yesu;
Tidzakomana naye Mkwatiyo.
[C]
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Yang’ana adza, yang’ana adza!
Konzeka akubwera Mkwatiyo.
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Yang’ana adza, yang’ana adza!
Konzeka akubwera Mkwatiyo.
[V4]
Tidzayimba mokondwera, Aleluya, kwa ’Ye;
Tidzayimba mokondwera, Aleluya, kwa ’Ye.
Yang’ana adza; yang’ana adza;
Yimbani, Aleluya, adzatu.
Tidzayimba mokondwera, Aleluya, kwa ’Ye;
Tidzayimba mokondwera, Aleluya, kwa ’Ye.
Yang’ana adza; yang’ana adza;
Yimbani, Aleluya, adzatu.
[C]
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Yang’ana adza, yang’ana adza!
Konzeka akubwera Mkwatiyo.
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Onani Mkwati, Yesu abweratu!
Yang’ana adza, yang’ana adza!
Konzeka akubwera Mkwatiyo.