Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #178

Hymn 178 Mmamawa Kapena Potuluka Dzuwa

[V1]
Mmamawa kapena potuluka dzuwa,
Ambuye Yesuyo ’dzafika ndi mphamvu,
Ndi ulemerero wo’kulu kutenga
Anthu ake mu dzikoli.

[C]
Yesu, Mbuye wathu,
’Dzayimba mokondwa liti?
Khristu adza, Khristu adza,
Aleluya amen. Aleluya amen.

[V2]
Kapena usana kapena madzulo,
Kapena usiku pamene Ambuye
’Dzafika mu ulemelero kutenga
Anthu ake mu dzikoli.

[C]
Yesu, Mbuye wathu,
’Dzayimba mokondwa liti?
Khristu adza, Khristu adza,
Aleluya amen. Aleluya amen.

[V3]
Tidzakondwa ngati tidzanka osafa,
Opanda kudwala, chisoni, maliro;
Kungokhwathulidwa podzadza kutenga
Anthu ake mu dzikoli.

[C]
Yesu, Mbuye wathu,
’Dzayimba mokondwa liti?
Khristu adza, Khristu adza,
Aleluya amen. Aleluya amen.

178. Mmamawa Kapena Potuluka Dzuwa

Link copied to clipboard successfully!