Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #91
Hymn 91 Linda Ndi Kupemphera
[V1]
Dikirani lero nthawi ili kutha;
Mungagwe m’zoipa linda ndi pemphero;
Thupi ndi lofoka mdaniyo ngwa mphamvu;
Dikirani nonse Mkwati ali kudza.
Dikirani lero nthawi ili kutha;
Mungagwe m’zoipa linda ndi pemphero;
Thupi ndi lofoka mdaniyo ngwa mphamvu;
Dikirani nonse Mkwati ali kudza.
[C]
Linda pempha, linda pempha;
Usiku ndi usana dikirani ndi kupemphera.
Linda pempha, linda pempha;
Usiku ndi usana dikirani ndi kupemphera.
[V1]
(Tenor and Bass):

[V2]
Dzukani m’sagone musamakaika;
Mudzalandiratu mpumulo kumwamba;
Linda ndi pemphero, Mpulumutsi wanu,
Anasautsidwa chifukwa cha inu

[V3]
Khulupira Yesu mdani ali pompo
Vala zida zako mpaka Mbuye adze,
Musachedwe konse lero ndi labwino,
Dikirani nonse ndi kupempheranso.