Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #137
Hymn 137 Dziko Ai, Koma Yesu
[V1]
Dziko ai, koma Yesu,
Dziko ndi lachabetu;
Nsisi zake zikhalitsa
Nthawi zonse yemweyo.
Dziko ai, koma Yesu,
Dziko ndi lachabetu;
Nsisi zake zikhalitsa
Nthawi zonse yemweyo.
[C]
Nsisi zake n’zazikulu,
Ndi chikondi chakenso;
Chiombolo chozizwitsa,
Moyotu wosathawo!
Nsisi zake n’zazikulu,
Ndi chikondi chakenso;
Chiombolo chozizwitsa,
Moyotu wosathawo!
[V2]
Dziko ai, koma Yesu,
Wondisangalatsa ’ne;
Iye andiyang’anira,
Nkana m’vuto ndi’mbabe.
Dziko ai, koma Yesu,
Wondisangalatsa ’ne;
Iye andiyang’anira,
Nkana m’vuto ndi’mbabe.
[C]
Nsisi zake n’zazikulu,
Ndi chikondi chakenso;
Chiombolo chozizwitsa,
Moyotu wosathawo!
Nsisi zake n’zazikulu,
Ndi chikondi chakenso;
Chiombolo chozizwitsa,
Moyotu wosathawo!
[V3]
Dziko ai, koma Yesu,
Ndiyang’ane Iyeyo;
Pa ulendo wanga wonse,
Andiunikira ’ne.
Dziko ai, koma Yesu,
Ndiyang’ane Iyeyo;
Pa ulendo wanga wonse,
Andiunikira ’ne.
[C]
Nsisi zake n’zazikulu,
Ndi chikondi chakenso;
Chiombolo chozizwitsa,
Moyotu wosathawo!
Nsisi zake n’zazikulu,
Ndi chikondi chakenso;
Chiombolo chozizwitsa,
Moyotu wosathawo!
[V4]
Dziko ai, koma Yesu,
Mtandawo ndigwiradi;
Mpakatu maso ndi maso,
Ndidzamone Mbuyeyo.
Dziko ai, koma Yesu,
Mtandawo ndigwiradi;
Mpakatu maso ndi maso,
Ndidzamone Mbuyeyo.
[C]
Nsisi zake n’zazikulu,
Ndi chikondi chakenso;
Chiombolo chozizwitsa,
Moyotu wosathawo!
Nsisi zake n’zazikulu,
Ndi chikondi chakenso;
Chiombolo chozizwitsa,
Moyotu wosathawo!