Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #45
Hymn 45 Patseni Bible
[V1]
GIVE ME THE BIBLE 1. Patseni Bible ndilo ndikufuna, Ndi chotitsogolera njirayo;
Monga mapiri oonetsa kwathu, Obweza anthu osocherawo.

[C]
Patseni Bible ndilo mau ake, Mau oyera a Mulunguyo,
Ndilo pangano la chikondi chake, ndi nyali mnjira yonka m’mwambamo.

[V2]
Patseni Bible ndilo ndikufuna, Mmene usweka mtima wangawo;
Patseni mau a Ambuye Yesu, Mau okondweretsa mmtimanga.

[V3]
Patseni Bible ndilo ndikufuna, Nyali ya kusonyeza njirayo,
Mmene ndingagwe lindipulumutsa, Lindisonyeza tchimo langalo.

[V4]
Patseni Bible ndilo ndikufuna, Liunikira a mu mdimawo,
Ndilo chiyembekezo kwa olira, Ndi nyali m’njira yonka m’mwambamo.