Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #136

Hymn 136 Akan’tsogoza Ndinkako

[V1]
Akan’tsogoza ndinkako,
Ndikhulupira Mbuyeyo;
Ndikumbukira kutitu
Anandifera pa mtanda.

[C]
Yesu anditsogozatu
Ulendo wanga wonsewo.
Bwenzi loona ndiyeyo,
Ndikumbukira Mtandawo.

[V2]
Ndikonda mau akewo,
Anditsogoze Mbuyeyo;
Kufuna kwake ndichite,
Anandifera pa mtanda.

[C]
Yesu anditsogozatu
Ulendo wanga wonsewo.
Bwenzi loona ndiyeyo,
Ndikumbukira Mtandawo.

[V3]
Ndzapita osaopai,
Akhale nane Yesuyo.
Pa tsiku lina n’dzaona
Yesu tsamwali wa mtanda.

[C]
Yesu anditsogozatu
Ulendo wanga wonsewo.
Bwenzi loona ndiyeyo,
Ndikumbukira Mtandawo.

136. Akan’tsogoza Ndinkako

Link copied to clipboard successfully!