Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #138
Hymn 138 Ndipereka Moyowu
[V1]
Ndipereka moyowu
Kwa Ambuye wanga ’Nu;
Manjawa achitetu
Chifuniro chanucho.
Ndipereka moyowu
Kwa Ambuye wanga ’Nu;
Manjawa achitetu
Chifuniro chanucho.
[C]
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
[V2]
Ndipereka miyendoyi,
Ikhaletu yanuyo;
Mau ayimbirenso
Inu Mfumu yangayo.
Ndipereka miyendoyi,
Ikhaletu yanuyo;
Mau ayimbirenso
Inu Mfumu yangayo.
[C]
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
[V3]
Ndipereka milomo,
Inenetu mauwo;
Ndipereka chumacho,
Sindimana kanthui.
Ndipereka milomo,
Inenetu mauwo;
Ndipereka chumacho,
Sindimana kanthui.
[C]
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
[V4]
Ndipereka nsikuzo,
Kuti ndiyamike ’Nu;
Ndipereka nzeruzo
Kuchitatu ntchitoyo.
Ndipereka nsikuzo,
Kuti ndiyamike ’Nu;
Ndipereka nzeruzo
Kuchitatu ntchitoyo.
[C]
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
[V5]
Chifuniro changacho
Chikhaletu chanunso;
Ndipereka mtimanga,
Ukhaletu wanunso.
Chifuniro changacho
Chikhaletu chanunso;
Ndipereka mtimanga,
Ukhaletu wanunso.
[C]
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
[V6]
Ndipereka chikondi
Pa mapazi anuwo;
Munditenge ndensene,
Ndikhaletu wanuyo.
Ndipereka chikondi
Pa mapazi anuwo;
Munditenge ndensene,
Ndikhaletu wanuyo.
[C]
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.
Munditsuke ine mtima mbu (E, ine mbu),
M’mwazi wa Ambuye Yesuyo (E, Yesuyo),
Kwanu Mbuyanga ndidziperekadi,
Kwanu nthawi zonsezo.