Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #114

Hymn 114 Chipata Chochinjikacho

[V1]
Chipata chochinjikacho, Chionetsera cheza;
Kuchokatu ku mtandawo, Chikondi chioneka.

[C]
Mwachinjikira ine ko, Chipata cha kumwambako?
Ine, Ine, Mwachinjikira ’ne?

[V2]
Chipata n’chauleretu Kwa onse akufuna;
Achuma, osaukanso, A mtundu uli wonse.

[C]
Mwachinjikira ine ko, Chipata cha kumwambako?
Ine, Ine, Mwachinjikira ’ne?

[V3]
Pitanitu mtsogolomo, Chipata n’chosatseka;
Landira mtanda wakewo, Mbonitu ya chikondi.

[C]
Mwachinjikira ine ko, Chipata cha kumwambako?
Ine, Ine, Mwachinjikira ’ne?

[V4]
Patsidya tidzatulapo, Mtandawo wa manyazi;
’Dzavalatu koronayo, ’Dzamkonda ’Ye koposa.

[C]
Mwachinjikira ine ko, Chipata cha kumwambako?
Ine, Ine, Mwachinjikira ’ne?

114. Chipata Chochinjikacho

Link copied to clipboard successfully!