Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #96
Hymn 96 Idza Tsiku Lopuma
[V1]
Idza tsiku lopuma, Lopatsidwa ku dziko.
Idza mmtima mwangamu, Monga nyali ya mmwamba.
Idza tsiku lopuma, Lopatsidwa ku dziko.
Idza mmtima mwangamu, Monga nyali ya mmwamba.
[V2]
Tsiku lokondweretsa, Likupita msangatu;
Litisangalatsanso Mpaka ntchito idzatha.
Tsiku lokondweretsa, Likupita msangatu;
Litisangalatsanso Mpaka ntchito idzatha.
[V3]
Tsiku loyeretsetsa, Tsiku lakupemphera;
Tsiku lakulandira madalitso anuwo.
Tsiku loyeretsetsa, Tsiku lakupemphera;
Tsiku lakulandira madalitso anuwo.
[V4]
Idza tsiku lopuma ndi zimphamvu za mmwamba,
Ndi kuyera kwanuko Kudze m’mtima mwangamu.
Idza tsiku lopuma ndi zimphamvu za mmwamba,
Ndi kuyera kwanuko Kudze m’mtima mwangamu.