Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #97
Hymn 97 Tamva Mau Omwewo
[V1]
Tamva mau omwewo, Atitu Yesuyo;
Mpulumutsi ndiyedi, Yesuyo, Yesuyo;
Pita m’midzi monsemo, Dziko lonse limvetu,
Pita iwe konseko, Mveratu Mbuyeyo.
Tamva mau omwewo, Atitu Yesuyo;
Mpulumutsi ndiyedi, Yesuyo, Yesuyo;
Pita m’midzi monsemo, Dziko lonse limvetu,
Pita iwe konseko, Mveratu Mbuyeyo.
[V2]
Lalikani nanunso, Yesuyo, Yesuyo;
Kwa ochima onsewo, Amve za mbuyeyo.
Lalikani m’zisimo, Ndi m’mapiri monsemo;
Kuti onse amvetu, Yesuyo, Yesuyo.
Lalikani nanunso, Yesuyo, Yesuyo;
Kwa ochima onsewo, Amve za mbuyeyo.
Lalikani m’zisimo, Ndi m’mapiri monsemo;
Kuti onse amvetu, Yesuyo, Yesuyo.
[V3]
Yimbadi za Iyeyo, Amvetu anthuwo;
Kuti Yesu wafadi, Kalelo, kalelo.
Atikonda ifetu, Natifera indedi.
Kuchotsera tchimoli, Yesuyo, Yesuyo.
Yimbadi za Iyeyo, Amvetu anthuwo;
Kuti Yesu wafadi, Kalelo, kalelo.
Atikonda ifetu, Natifera indedi.
Kuchotsera tchimoli, Yesuyo, Yesuyo.
[V4]
Bukitsani maunso, Konseko, konseko.
Aitana anthuwo, Ponsepo, ponsepo.
Kodi wina samvatu? Pitako, pitako ’we,
Angofuna onsewo, Yesuyo, Yesuyo
Bukitsani maunso, Konseko, konseko.
Aitana anthuwo, Ponsepo, ponsepo.
Kodi wina samvatu? Pitako, pitako ’we,
Angofuna onsewo, Yesuyo, Yesuyo