Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #92

Hymn 92 Msaiwale Tsiku La Mbuye

[V1]
Msaiwale tsiku la Mbuye wathuyo.
Ndi tsiku lopambana masiku enawo;
Ndi tsiku lakupuma ndi la chimwemwecho,
Kuwala kwake kuli kochoka mmwambamo.

[C]
Tikondwera kudza kwa Sabata lakelo.
Tikondwera kudza kwa Sabata lakelo.

[V2]
Sunga tsiku lake lopatulikalo,
Pembedza mwini njira yakunka mmwambamo;
Tikamtsatira Iye pa dziko linotu,
Adzatipatsa madzi a moyo wakewo.

[C]
Tikondwera kudza kwa Sabata lakelo.
Tikondwera kudza kwa Sabata lakelo.

[V3]
Timyimbira Yesu pa tsiku lonseli,
Ambuye ali Bwenzi la ana onsewo.
Wokoma mtima ndinu, Mukhale nafetu,
Munalonjeza kuti mudzadza m’mtimamu.

[C]
Tikondwera kudza kwa Sabata lakelo.
Tikondwera kudza kwa Sabata lakelo.

92. Msaiwale Tsiku La Mbuye

Link copied to clipboard successfully!