Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #90
Hymn 90 Ntchito Ya Pa Mlungu Yatha
[V1]
Ntchito ya pa mlungu yatha,
Sabata lina layamba;
Moyo wangawe pumula,
Mlungu wadalitsa lero.
Ntchito ya pa mlungu yatha,
Sabata lina layamba;
Moyo wangawe pumula,
Mlungu wadalitsa lero.
[V2]
Idza yamika Ambuye,
Yemwe apatsa mpumulo;
Timadalitsidwa lero,
Koposa masiku ena.
Idza yamika Ambuye,
Yemwe apatsa mpumulo;
Timadalitsidwa lero,
Koposa masiku ena.
[V3]
Mayamiko athu m’mwamba,
Akweratu monga nsembe;
Kuti Khristu atipatse
Dalitso m’mitima yathu.
Mayamiko athu m’mwamba,
Akweratu monga nsembe;
Kuti Khristu atipatse
Dalitso m’mitima yathu.
[V4]
Mpumulowu uli ngati
Fanizo la wakumwamba,
Komwe mpingo udzapuma,
Zitatha zowawa zonse.
Mpumulowu uli ngati
Fanizo la wakumwamba,
Komwe mpingo udzapuma,
Zitatha zowawa zonse.