Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #70
Hymn 70 Tidzaima Bwanji Pa Chiweruzo?
[V1]
WHEN JESUS SHALL GATHER 1. Mmene Yesu adzasonkhatu, Mitundu yonse ya dziko,
Kodi tidzaima bwanji’fe Pa mpando wachiweruzo?

[C]
Adzasonkhanitsa tiriguyo, Koma mankhusu adzataya;
Nanga tidzaima bwanji ko’ Pa tsiku la chiweruzo?
2. Kodi tidzamva mau ake, Wachita bwino iwetu,
Kapena tidzanjenjemera, Tidzachotsedwa ku mpando?
3. Iye adzakondwera ndithu, Kuona owomboledwa,
Adzawabvekatu zobvala, Pa kugwadira Mbuyeyo.
4. Tiyeni tidikire tsono, Ndi nyali zathu zowala,
Poitana Mkwati ku phwando Tidzakhale okonzeka.
5. Tikakhala okonzekatu, Tikakhala opirira;
Podzatha ulendo wathuwu, Tidzanka naye kumwamba.